
Kudabwa Nthawi zina ndima dabwa Wanga anthu momwe ama khala Kubaba mtima wanga uma baba Ubaba anthu zomwe ama panga Kudana anthu awa ama dana Sibanja ine mango khala Mwina ndi nyanga zomwe wina ana panga Kapena sinyanga nakuba kapena chabe nikaduka Kamene kalengesa banthu bamozi kupeza vifukwa Cifukwa mayeso fufuza koma sina peze cifukwa eh Kunjako nko kudha macita mantha ndi khalidwe yawa Udani waconco wacoka kuti ma lankhulana Pempelo yanga niyoti izozo ma lalilane Nanga cikondi munali naco cinapita kuti Funso Kudabwa Nthawi zina ndima dabwa Wanga anthu momwe ama khala Kubaba mtima wanga uma baba Ubaba anthu zomwe ama panga Kudana anthu awa ama dana Sibanja ine mango khala Kumakhalila midesu Ena akulila Yesu Mundisamalile ana banja isa pwasuke tikhale ifeso Ogwilizana despite what we facing I hope we don’t break us ineo Pemphelo yanga ndiyoti udani ulipo kuntima uthepo Koma zukhala nga e sizotheka anthuwa afuna afepo Udani waconco ku opya Ambuye kumwamba muyanganilepo Kuma kangana pa zopanda phindu poka poka ena afepo Anthu wa ndani aloza umbuli wa conci ine sina onepo Kudabwa Nthawi zina ndima dabwa Wanga anthu momwe ama khala Kubaba mtima wanga uma baba Ubaba anthu zomwe ama panga Kudana anthu awa ama dana Sibanja ine mango khala
Песен-НИКИ
Загрузка...
Похожие песни

Бигасс
SODA LUV
Ничего личного
Русский рэп201975,446

Бандана
Платина
РНБ КЛУБ
Русский рэп201859,980

Свадебное путешествие
Александр Буйнов
Острова любви
Русская эстрада199954,906

Каспий жағалауы
Azamat
Поп200134,438

Шпилька-каблучок
Лолита
Анатомия
Русская эстрада201433,308

Девочка 2D
Dead Rave
Singles 15-17
Русский рэп201828,891